Miyambo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wabwino Yehova amakondwera naye,+ koma munthu wamaganizo oipa iye amamutcha woipa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:2 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, tsa. 28