Miyambo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Maganizo a anthu olungama ndiwo chilungamo.+ Utsogoleri wa anthu oipa ndi wachinyengo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, tsa. 30