Miyambo 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mlomo wa choonadi+ ndi umene udzakhazikike kwamuyaya,+ koma lilime lachinyengo lidzangokhalapo kwa kanthawi.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:19 Nsanja ya Olonda,2/1/2007, tsa. 73/15/2003, tsa. 28
19 Mlomo wa choonadi+ ndi umene udzakhazikike kwamuyaya,+ koma lilime lachinyengo lidzangokhalapo kwa kanthawi.+