Miyambo 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chikwapu cha kudzikuza chili m’kamwa mwa wopusa,+ koma anthu anzeru milomo yawo imawatsogolera.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:3 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 27