Miyambo 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu wonyoza amafunafuna nzeru ndipo sazipeza. Koma kudziwa zinthu kumakhala kosavuta kwa munthu womvetsa zinthu.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, ptsa. 28-29
6 Munthu wonyoza amafunafuna nzeru ndipo sazipeza. Koma kudziwa zinthu kumakhala kosavuta kwa munthu womvetsa zinthu.+