Miyambo 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu wa mtima wosakhulupirika adzakhutira ndi zotsatira za njira zake,+ koma munthu wabwino adzakhutira ndi zotsatira za zochita zake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:14 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, tsa. 185/15/1987, tsa. 29
14 Munthu wa mtima wosakhulupirika adzakhutira ndi zotsatira za njira zake,+ koma munthu wabwino adzakhutira ndi zotsatira za zochita zake.+