Miyambo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu oipa adzagwadira abwino,+ ndipo oipa adzagwada pazipata za munthu wolungama. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:19 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, ptsa. 19-20