Miyambo 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu okonza chiwembu amasochera,+ koma anthu okonzekera kuchita zabwino amapeza kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:22 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, tsa. 20
22 Anthu okonza chiwembu amasochera,+ koma anthu okonzekera kuchita zabwino amapeza kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+