Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:29 Nsanja ya Olonda,9/15/2005, tsa. 143/15/1997, ptsa. 13-149/15/1990, tsa. 22
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+