Miyambo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Siliva amamuyengera m’mbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera m’ng’anjo,+ koma Yehova ndiye amene amayesa mitima.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:3 Galamukani!,8/8/1990, tsa. 15
3 Siliva amamuyengera m’mbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera m’ng’anjo,+ koma Yehova ndiye amene amayesa mitima.+