Miyambo 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wa mtima wopotoka sadzapeza zabwino,+ ndipo wa lilime lokhota adzagwera m’tsoka.+