Miyambo 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Bambo wa mwana wopusa amamva chisoni,+ ndipo bambo wa mwana wopanda nzeru sasangalala.+