Miyambo 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwana wopusa amakhumudwitsa bambo ake,+ ndipo amamvetsa chisoni mayi ake amene anam’bereka.+