Miyambo 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kukondera munthu woipa si bwino.+ Komanso si bwino kukankhira pambali munthu wolungama poweruza.+