Miyambo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtima wa munthu womvetsa zinthu umadziwa zinthu,+ ndipo khutu la anzeru limafunafuna kudziwa zinthu.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:15 Nsanja ya Olonda,10/15/2004, ptsa. 14-15
15 Mtima wa munthu womvetsa zinthu umadziwa zinthu,+ ndipo khutu la anzeru limafunafuna kudziwa zinthu.+