Miyambo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa ndiye dipo la wolungama,+ ndipo munthu wochita zachinyengo amalowa m’malo mwa anthu owongoka mtima.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:18 Mtendere Weniweni, ptsa. 40-41
18 Munthu woipa ndiye dipo la wolungama,+ ndipo munthu wochita zachinyengo amalowa m’malo mwa anthu owongoka mtima.+