Miyambo 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chuma chosiririka ndiponso mafuta zimakhala pamalo a munthu wanzeru,+ koma wopusa amazimeza.+