Miyambo 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsiku lonse amaoneka kuti akulakalaka kwambiri chinachake, koma wolungama amapatsa ndipo saumira chilichonse.+
26 Tsiku lonse amaoneka kuti akulakalaka kwambiri chinachake, koma wolungama amapatsa ndipo saumira chilichonse.+