Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:30 Nsanja ya Olonda,3/15/1997, ptsa. 15-16