Miyambo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wolemera ndiponso munthu wosauka n’chimodzimodzi.+ Amene anapanga onsewa ndi Yehova.+