Miyambo 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Minga ndi misampha zimakhala m’njira ya munthu wochita zopotoka,+ koma woteteza moyo wake amakhala nazo kutali.+
5 Minga ndi misampha zimakhala m’njira ya munthu wochita zopotoka,+ koma woteteza moyo wake amakhala nazo kutali.+