Miyambo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofesa zosalungama adzakolola zopweteka,+ ndipo ndodo ya ukali wake idzatha.+