Miyambo 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Thamangitsa wonyoza, kuti mikangano ithe ndiponso kuti milandu ndi kunyozedwa zilekeke.+