Miyambo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usamadye chakudya cha aliyense womana,+ kapena kusonyeza kuti ukulakalaka zakudya zake zokoma.+