Miyambo 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bweretsa mtima wako kuti umve malangizo, ndi khutu lako kuti limve mawu a munthu wodziwa zinthu.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:12 Nsanja ya Olonda,7/1/2006, tsa. 13