Miyambo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Usam’mane chilango* mwana.+ Ngakhale utam’kwapula ndi chikwapu, sangafe ayi.