Miyambo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtima wako usamasirire anthu ochimwa,+ koma iwe uziopa Yehova tsiku lonse.+