Miyambo 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa ukatero udzakhala ndi tsogolo labwino,+ ndipo chiyembekezo chako sichidzawonongedwa.+