Miyambo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usamasirire anthu oipa,+ ndipo usamasonyeze kuti ukusirira kukhala pagulu lawo,+