Miyambo 24:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo ndinaona kuti munali tchire lokhalokha.+ Zitsamba zoyabwa zinali paliponse m’mundamo komanso mpanda wake wamiyala unali utagumuka.+
31 Ndipo ndinaona kuti munali tchire lokhalokha.+ Zitsamba zoyabwa zinali paliponse m’mundamo komanso mpanda wake wamiyala unali utagumuka.+