Miyambo 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mbalame imakhala ndi chifukwa chothawira, ndiponso namzeze* amakhala ndi chifukwa choulukira. Momwemonso temberero silibwera popanda chifukwa chenicheni.+
2 Mbalame imakhala ndi chifukwa chothawira, ndiponso namzeze* amakhala ndi chifukwa choulukira. Momwemonso temberero silibwera popanda chifukwa chenicheni.+