Miyambo 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzudzula munthu mosabisa mawu, kuli bwino+ kusiyana ndi kumukonda koma osamusonyeza chikondicho.