Miyambo 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Monga mbalame imene ikuthawa pachisa pake,+ ndi mmenenso amakhalira munthu amene akuthawa kwawo.+