Miyambo 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Udzu wobiriwira wapita, udzu watsopano waoneka, ndipo zomera za m’mapiri zasonkhanitsidwa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:25 Nsanja ya Olonda,8/1/1991, tsa. 31