Miyambo 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nkhosa zamphongo zazing’ono zimakupezetsa zovala,+ ndipo mbuzi zamphongo ndizo malipiro ogulira munda. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:26 Nsanja ya Olonda,8/1/1991, tsa. 31
26 Nkhosa zamphongo zazing’ono zimakupezetsa zovala,+ ndipo mbuzi zamphongo ndizo malipiro ogulira munda.