Miyambo 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wantchito salola kusintha ndi mawu okha,+ chifukwa amamvetsa koma satsatira.+