Miyambo 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi waona munthu wopupuluma m’mawu ake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu kuposa iyeyo.+
20 Kodi waona munthu wopupuluma m’mawu ake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu kuposa iyeyo.+