Miyambo 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu wopanda chilungamo amakhala wonyansa kwa anthu olungama,+ ndipo munthu wowongoka m’njira yake amakhala wonyansa kwa munthu woipa.+
27 Munthu wopanda chilungamo amakhala wonyansa kwa anthu olungama,+ ndipo munthu wowongoka m’njira yake amakhala wonyansa kwa munthu woipa.+