Miyambo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:9 Nsanja ya Olonda,9/15/1997, tsa. 311/15/1990, ptsa. 5-6 Galamukani!,11/8/1997, tsa. 21
9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+