Mlaliki 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+
8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+