Mlaliki 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:11 Nsanja ya Olonda,9/1/2010, tsa. 4 Mtendere Weniweni, tsa. 135
11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+