Mlaliki 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mogwirizana ndi zimenezi ndinatsimikiza mumtima mwanga+ kuti ndidziwe nzeru ndiponso ndione ntchito imene ikuchitika padziko lapansi,+ chifukwa alipo amene sagona tulo usana ndi usiku.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:16 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 16
16 Mogwirizana ndi zimenezi ndinatsimikiza mumtima mwanga+ kuti ndidziwe nzeru ndiponso ndione ntchito imene ikuchitika padziko lapansi,+ chifukwa alipo amene sagona tulo usana ndi usiku.+