Mlaliki 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Panali mzinda winawake waung’ono ndipo mumzindamo munali amuna ochepa. Kenako kunabwera mfumu yamphamvu ndipo inazungulira mzindawo, n’kuunjika milu ikuluikulu yadothi yoti imenyerepo nkhondo.+
14 Panali mzinda winawake waung’ono ndipo mumzindamo munali amuna ochepa. Kenako kunabwera mfumu yamphamvu ndipo inazungulira mzindawo, n’kuunjika milu ikuluikulu yadothi yoti imenyerepo nkhondo.+