Mlaliki 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ineyo ndinati: “Nzeru n’zabwino kuposa mphamvu,+ koma nzeru za munthu wosauka zimanyozedwa ndipo anthu samvera mawu ake.”+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:16 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, tsa. 32
16 Choncho ineyo ndinati: “Nzeru n’zabwino kuposa mphamvu,+ koma nzeru za munthu wosauka zimanyozedwa ndipo anthu samvera mawu ake.”+