Mlaliki 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dziko iwe, ndiwe wodala ngati mfumu yako ili mwana wochokera ku banja lachifumu, ndipo akalonga ako amadya pa nthawi yake kuti akhale amphamvu, osati kumangomwa mopitirira muyezo.+
17 Dziko iwe, ndiwe wodala ngati mfumu yako ili mwana wochokera ku banja lachifumu, ndipo akalonga ako amadya pa nthawi yake kuti akhale amphamvu, osati kumangomwa mopitirira muyezo.+