Nyimbo ya Solomo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musandiyang’anitsitse chifukwa chakuti ndada, ndi dzuwatu landidetsali. Pakuti ana aamuna a mayi anga anandikwiyira. Choncho anandiika kuti ndiziyang’anira minda ya mpesa moti sindinathe kuyang’anira munda wangawanga wa mpesa.+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,1/15/2015, tsa. 32 Galamukani!,4/8/1994, ptsa. 24-25
6 Musandiyang’anitsitse chifukwa chakuti ndada, ndi dzuwatu landidetsali. Pakuti ana aamuna a mayi anga anandikwiyira. Choncho anandiika kuti ndiziyang’anira minda ya mpesa moti sindinathe kuyang’anira munda wangawanga wa mpesa.+