Nyimbo ya Solomo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pamene mfumu yakhala patebulo lake lozungulira, fungo labwino la nado*+ wanga likumveka kwa wokondedwa wanga.+
12 “Pamene mfumu yakhala patebulo lake lozungulira, fungo labwino la nado*+ wanga likumveka kwa wokondedwa wanga.+