Nyimbo ya Solomo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero ndinati: ‘Ndidzuke ndikazungulire mumzinda,+ m’misewu ndi m’mabwalo a mumzinda,+ kuti ndikafunefune munthu amene mtima wanga umam’konda.’ Ndinam’funafuna koma sindinamupeze.
2 Chotero ndinati: ‘Ndidzuke ndikazungulire mumzinda,+ m’misewu ndi m’mabwalo a mumzinda,+ kuti ndikafunefune munthu amene mtima wanga umam’konda.’ Ndinam’funafuna koma sindinamupeze.