Nyimbo ya Solomo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakulumbiritsani inu+ ana aakazi a ku Yerusalemu, pali mbawala zazikazi ndiponso pali mphoyo zakutchire,+ kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.”+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,1/15/2015, tsa. 3111/15/2006, ptsa. 18-1911/15/1987, ptsa. 24-25
5 Ndakulumbiritsani inu+ ana aakazi a ku Yerusalemu, pali mbawala zazikazi ndiponso pali mphoyo zakutchire,+ kuti musayese kudzutsa chikondi mwa ine mpaka pamene chikondicho chifunire.”+