-
Nyimbo ya Solomo 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mizati yake ndi yasiliva. Motsamira mwake ndi mwagolide. Pokhalira pake ndi popangidwa ndi ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira. Mkati mwake, ana aakazi a ku Yerusalemu akongoletsamo posonyeza chikondi.”
-